Ophunzira ku Kasungu alonjezedwa thandizo
Ophunzira omwe asankhidwira m’sukulu za sekondale za boma ku Kasungu, alonjezedwa kuti palibe asiyire sukulu panjira kaamba kosowa ndalama za fizi.Izi ndi malingana ndi phungu wa dera lapakati m’boma la Kasungu, Chikondi Kampachike Chisale yemwe wati awonetsetsa kuti ophunzira ochepekedwa adzithandizidwa kudzera mu thumba la ndalama zakudera (CDF) kuti asalephere maphunziro awo kaamba ka umphawi.A...Chayamba Secondary·Chikondi Kampachike Chisale