Skip to content
Standard
Reader
Log in
Tag
Chichewa
Articles and publications tagged Chichewa across the Atmosphere.
2
articles
1
publication
Articles
Publications
Recent
Recent
Trending
Most popular
Malawi24
·
Oct 21, 2026
Mjigo wakana kukonzedwa ku Kasungu
Agwidwa njakata aphunzitsi ndi ophunzira pa sukulu ya Nthema Primary, kudera la mfumu yaikulu Wimbe ku Kasungu komwe mjigo sukumva kukonzedwa. Pomwe azanyengo akulimbikitsa anthu kumwa madzi pafupifu pafupi kamba ka kutentha konyanyira, kupeza madziwa pakati pa ophunzira pa sukuluyi ndi ntchito ya padera kamba ka mjigowu omwe tsopano ndi bwenzi la mphasa. Malingana ndi...
Chichewa
·
Kasungu Mjigo
Malawi24
·
Oct 20, 2026
A Namalomba akufuna umboni ngati ndani? – Suleman
Kwakhwithima! Ndipo mawere awirirana! Kusagwirizana kwa akuluakulu aboma kwafika mlingo wina tsopano pomwe sipikala wa nyumba yamalamulo, Sameer Suleman wabweza moto kwa a Shadric Namalomba. “Kodi a Namalomba akufuna umboni ngati ndani? A Namalomba asanduka liti wapolisi kapena wa ACB? Awa ndi ena mwa mafunso omwe achoka kwa sipikala kupita kwa nduna yofalitsa nkhaniyi. Chatsitsa...
Chichewa
·
Kstsngsle
You've reached the end.
Home
Latest
Discover
Search