Wanderers isamadalire kuyibereka — Mtawali
Mphunzitsi wa timu ya CRECK Sporting Club, Enerst Mtawali wati kukonderedwa kwa matimu ena mdziko muno, ndi china mwa zifukwa zomwe zikupangitsa kuti timu ya dziko lino isamachite bwino.Mtawali amayankhula izi pa bwalo la zamasewero la Mpira mu mzinda wa Blantyre pomwe timu yake yagonja kwa Mighty Wanderers ndi chigoli chimodzi kwa duu chomwe anagoletsa...Ernest Mtawali·FDH Premiership