Kukana kuvala chipewa pa kabanza kukuonongetsa chuma chaboma — Ben Phiri
Nduna ya zamaboma ang'ono, Ben Phiri yadzudzula anthu omwe amakana kuvala chipewa chodzitetezera akakwezedwa njinga za kabanza, ponena kuti khalidweli likuthandizira kuonongeka kwa chuma cha boma. Phiri wati boma likuyesetsa kuti ngozi za njinga za moto zichepe koma pali anthu ena omwe salabadira izi ndipo akumasankha kusatsatira malamulo.Ndunayi yati chokhumudwitsa kwambiri ndichoti ngozi zikachitika boma...Ben Phiri·Kabanza