Chipasupasu! A Malawi a sambwadza Namalomba
… aMalawi ali nganganga pambuyo pa Suleman Yatangwanika zedi nduna yofalitsa nkhani a Shadric Namalomba kuikira kumbuyo akuluakulu aboma pa nkhani yoti nduna ndi akuluakulu ena akususa kwambiri pa ndalama za misonkho ya a Malawi. Koma aMalawi sakugwirizana ndi ganizoli. Posachedwapa, sipikala wa nyumba ya malamulo Sameer Suleman, adayankhula pa mwambo wina kudzudzula mchitidwe waumbava...Anti-Corruption Bureau (ACB)·corruption