Ena akuikira kumbuyo bambo wokumba manda ake
Pomwe kwa ena ndi mwikho, ambiri maka pa masamba amchezo ati sakuwonapo vuto ndi zomwe ikuchita njonda ina ku Dowa yomwe ikukumbiratu dzenje lomwe anthu ambiri safuna ataliwona.Faidoni Benamu Kalitsiro wazaka 78, wadodometsa anthu pomwe wayamba ntchito yokumba manda ake m'mudzi wa Makwani m'dera la mfumu yayikulu Dzoole m'bomali.Benamu Kalitsiro wati ntchito yokumba mandawa ikuyembekezeka...Dowa·Faidoni Benamu Kalitsiro