Kusuta bositiki, m’buka kwakula kwa Chemusa
Pali chiopsezo kuti chiwerengero cha achinyamata ozungilira mitu chitha kukwera kwambiri kudera la Chemusa munzinda wa Blantyre komwe akuti mchitidwe osuta bositiki omatira zinthu komaso miyala ya m'buka wafika posauzana.Fred Msiyambiri yemwe ndi khansala wa wadi ya Mussa-Magasa anadandaula zakukula kwa mchitidwewu pa maliro ena mderali Lachitatu sabata ino, komwe anachonderera achinyamata kuti asiye.Titamukokera pambali...Counsellor Fred Msiyambiri·Drug and substance Abuse