Pepani aMalawi tikukugonekani mu mdima — Namalomba
Nduna yofalitsa nkhani yemwenso ndi m'neneri wa boma a Shadric Namalomba apepesa mtundu wa aMalawi chifukwa cha kuzimazima kwa magetsi komwe kukuchitika mdziko lino.A Namalomba ati boma likuvomereza kuti likuwagoneka anthu mu mdima.Polankhula ndi wayilesi ya kanema ya Zodiak loweluka a Namalomba ati kuzimazima kwa magetsi ndi vuto lalikulu lomwe akuyesesa kuthana nalo."Mwina timachitika tsoka,...Shadreck Namalomba·National