Bambo wagamulidwa pogulitsa malonda malo olakwika
Kugulitsa apozi pa Nandozi munzinda wa Blantyre kwalanga bambo wina yemwe khothi lamugamula kuti apereke chindapusa, apo bii akalowe kumpanda.Bwalo la mirandu la Magistrate mu mzinda wa Blantyre lagamula Lawrence James kupereka chindapusa cha K20,000 kapena kukaseweza jere kwa miyezi 12, kaamba kopezeka akugulitsa apozi (apples) malo osayenera.A Kingsley Matope, omwe ndi oyimira boma pa...BCC·Blantyre City Council (BCC)