Tikupwetekani — Mpuluka waopseza andale
…wati agwiritsa ntchito mtera …nawo onyoza Mutharika achenjezedwa Mukumanyoza m’tsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika? Samalani. Ku mwambo wa Mulhako wa Alhomwe wa chaka chino kwatuluka chenjezo lomwe akuti ngati sizisintha mutha nonse psiti! Apo bii kum’mwera mukuvera fungo. Wapampando wa Mulhakho wa Alhomwe, Muchanakwaye Mpuluka, wachenjeza anthu onse omwe akumasokoneza chikhalidwe cha Chihlomwe komanso...Chonde Mulanje·Muchanakwaye Mpuluka