Zipembedzo m’dziko muno zimaloleza kuchotsa mimba
Ngakhale kwa nthawi yayitali pakhala mtsutso pa malamulo a dziko lino komaso a zipembedzo ngati n'koyenera kuti amai ndi atsikana adzichotsa mimba, kafukufuku wapeza kuti dziko lino komaso mipingo izi ndizololedwa.Izi zadziwika lachiwiri pa maphunziro omwe bungwe lopereka ntchito zokhudza umoyo wa uchembere, kulera, komanso zaumoyo wa amayi ndi ana, la Banja la Mtsogolo linakonzera...Abortion·Kuchotsa mimba m'Malawi