Skip to content
Standard
Reader
Log in
Tag
Nyama Ya Galu
Articles and publications tagged Nyama Ya Galu across the Atmosphere.
2
articles
1
publication
Articles
Publications
Recent
Recent
Trending
Most popular
Malawi24
·
Aug 18, 2026
Zaka zitatu kundende pogulitsa nyama yagalu
Ikakuona litsiro sikata, mkulu uja amkamuzenga mlandu ogulitsa nyama ya galu ku Kasungu, tsopano amugamula kukaseweza jere kwa zaka zitatu.Bwalo la milandu la Chief Resident Magistrate m'bomali lapeza olakwa mkuluyu emwe dzina lake ndi Juma Fabiano wazaka 49 pa mulandu wogulitsa nyama yagalu.Izi zichitika ngakhale adayithyola m'maso muli gwaa powuza bwalo la milandu kuti adapha...
Crime
·
Dog meet
Malawi24
·
Jul 23, 2026
Wogulitsa nyama ya galu wayithyola mukhothi
Njonda yomwe ikuyankha mlandu ogulitsa nyama ya galu ku Kasungu, inayithola m'maso muli gwa mukhothi pomwe inati inapha galuyo osati kuti igulitse.Juma Sabiano wa zaka 49, wam'mudzi mwa Chisinga m’bomali, wamayankhula izi podzitetezera pa mlanduwu pamene amaonekera ka chiwiri ku bwalo la mirandu. Sabiano ndi mzawo Chisomo Willard adanjatwa mwezi wa June m'mudzi mwa Chisinga...
Crime
·
Galu
You've reached the end.
Home
Latest
Discover
Search