Zomwe zinachitikapo kale sizingapose malamulo a dziko: MLS ikukhonza
Bungwe la Malawi Law Society (MLS) liyenera kusapotedwa chifukwa chotsutsa ganizo la Pulezidenti Peter Mutharika loyimitsa yekha msonkhano wa Nyumba ya Malamulo wokambirana za momwe bajeti ya chaka cha 2026 ikuyendera pakati pa chaka. Maganizo a bungweli sakukhudzana ndi kukondera zipani za ndale. Cholinga chake ndi kuteteza malamulo oyendetsera dziko komanso kuonetsetsa kuti palibe Pulezidenti...Bingu wa Mutharika·Chichewa