Wanjinga wafa pothawitsa mafuta kwa apolisi
Woyendetsa njinga yamoto yemwe ananyamula zigubu zamafuta a galimoto, wafa atagwa ndikuyaka moto pomwe amathamangitsidwa ndi a polisi. Malingana ndi yemwe tawona pa tsamba la Facebook, izi zachitika pa Kanengo mu mzinda wa Lilongwe. Mu kanemayu mukuveka mau a yemwe amajambula ndipo wafotokoza kuti wanjingayu amathawa galimoto yapolisi yomwe imamuthangitsa, koma anakagwera kutchire komwe moto...Fuel shortages·Motorcycle Accident